[male vocals] Zambia
tamva,
tamva!
Ayi,
yoh,
tiyeni!
[male vocals] Zambia
tamva,
tamva!
Ayi,
yoh,
tiyeni!
Azambia
asekelera,
anthu
ali
m'sewera
Chilungamo
chasowa,
mtima
ukuwawa
Musiileni
Mulungu,
iyeyu
wodziwa
Amsiye
ndi
alimi,
akondwa
ndi
mtsogoleri
Ena
alira
kodi,
chilungamo
casowa
Koma
ife
tilinso,
tili
m'manja
mwa
Mulungu
Zikatere
bwanji,
sitidziwa
kodi
Sikufuna
kwathu,
ai,
ai
Ndi
kwanu
Ambuye,
musunge
dziko
lino
Nthawi
yafika,
tiyeni
tipemphere
Titeteze
Hakainde,
tiyeni
tikhulupirire
Titeteze
Mundubile,
Ambuye
onetsetsani
Chilungamo,
chilungamo
chikhale
pansi
Amene
apambana,
ndi
kufuna
kwanu
Onse
ndife
azambia,
palibe
kusankhana
Hakainde,
Mundubile,
onsewa
ndi
anthu
Makebi
onsewo,
ndimafumu
athu
kodi
Tikufuna
mtendere,
tikufuna
umodzi
Nthawi
yafika,
tiyeni
tipemphere
Titeteze
Hakainde,
tiyeni
tikhulupirire
Titeteze
Mundubile,
Ambuye
onetsetsani
Chilungamo,
chilungamo
chikhale
pansi
ECZ
yalakwa,
makhoti
yalakwa
kodi
Tisiile
Mulungu,
nkhondo
si
yathu
Sikuti
nkhondo
yathu,
ndi
nkhondo
ya
Mulungu
Ayi,
yoh,
tamva!
Nthawi
yafika,
tiyeni
tipemphere
Titeteze
Hakainde,
tiyeni
tikhulupirire
Titeteze
Mundubile,
Ambuye
onetsetsani
Chilungamo,
chilungamo
chikhale
pansi
Ambuye
mucionetse,
chilungamo
kwa
onse
Kufuna
kwanu
kucitidwe,
Ambuye
lero
Apostle
Lungu
Esau,
tamva!
Zambia,
tisunge
umodzi,
ayi!