[male
vocals] (
Choir
humming
softly
in
harmony) (
Piano
building
momentum)
Oh,
Mvelani
nyimbo
yokuongani
Ambeye.
Nikweza
maso
anga
kumwamba
Tikweza
mau ,
tikufuula
kwa
Ambeye.
Ambuye,
Nati
zikomo
pa
chikondi
canu
cachikulu.
Muniyanganila
zocita
zanga,
municinjiliza
ku
zoipa
chifukwa
ca
moyo
wanga
mwanipasa
Cakudya
canga
munipasa
nthawi
zonse
Munipasaso
pousila
Mwazaza
moyo
wanga
Ndimadali
ambiri-mbiri
Ni
paname
nji
pa
inu
Ambuye
Zikomo,
zikomo,
ndimvereni
Ninena
zikomo
kwainu,
Ambuye,
ponimasula
Pa
moyo
wanga
mwandipasa,
utuba
komanso
wong'enzimira
ngati
nthanda
Ndikuyenda
pasogolo
mkuwala
kwanu
Ndiimba,
Hallelujah,
Hallelujah
kwa
inu
Mbuye
wanga,
ndi
Mulungu
wanga,
ndipita
pasogolo
Pa
nzelu
zakuya
mwaika
pa
ine
Ndi
maluso
ambiri-mbiri
muli
ku
ndi
sogolela
Pamene
ndi
pita
mu
ziphunziso
Pa
chisomo
mwakhoza
kuthira
pa
mutu
panga
Ndi
madaliso
osawerengeka
Moyo
wanga
kuyenda
bwino-bwino
ngati
madzi
Ndigoneka
mtima
wanga
pa
maphazi
anu
Kuyamika
kwanga
ni
kwa
chendi
ndipo
nokonzuna
Zikomo,
zikomo,
ndimvereni
Ninena
zikomo,
Ambuye,
po
ndimasula
Pa
moyo
wanga
mwanipasa,
woyera
ndipo
wong'enzimira
Ndipita
pa
sogolo
mu
madaliso
anu
Ndiimba
Hallelujah,
Hallelujah
kwa
inu
Mbuye
wanga,
ndi
Mulungu
wanga,
mukuona
ndipita
pasogolo (
Building
intensity)
Kucokela
komwe
dzuwa
itulukila
Kupita
komwe
ilowela
Cikondi
canu,
Ambuye,
sicisila (
Choir
swelling,
powerful
harmony)
Takweza
manja,
takweza
mitima
yathu
Ku
zabwino ,
lekani
zabwino
ziyambe
kucita
nase
Zikomo,
zikomo,
ndimvereni
Ndinena
zikomo ,
Ambuye,
ponimasula
Pa
moyo
mwanipasa,
woyera
ndipo
wong'enzimira
Ndipita
pasogolo
mu
madaliso
anu
Ndiimba
Hallelujah,
Hallelujah
kwa
inu
Ambuye
wanga,
ndi
Mulungu
wanga,
ndiku
pitililabe
pa
sogolo. (
Music
calming
down)
Shout
out
to
one
Mando,
K.
O
My
first
son
Nono
Ba
Givo,
Richmond,
Evans
Jr
Zacks,
Aaronzo,
and
one
BM
This
is
the
mix,
let
the
praises
rise
Thank
you
Lord,
Hallelujah (
Fade
out
with
choir
harmony)