M'mamawa kukacha...!!"
Ndimagwada pansi"
kuthokoza mbuye" mbuye wanga zikomo...!!"
Sim'nali mkudziwa inee..! Kuti ndingadzuke tawonani lero mwandidzutsa ndimoyo..!"□
Tinali mkucheza dzulo" ndi-azanga ena!!" Pamene kukucha ndikumva kuti maliro.
Zandigwetsa mphwayi....!!" zandi-lilitsa poona zanga uja kuti lero wamwalira...!!
Ndangozindikila" kuti dzikoli... dzikoli la pansi-li ndilovuta.
Chorus
Dzikoli la pansili....!!"
Dziko la pansi-li....!!"
Dziko la pansi iwe ndilovuta ukalitengela udzafa usanalape" dziko la pansi mzanga ndilovuta ukalitengela udzafa usalape.
M'bale wanga lapa machimo akowo" chifukwa nthawi yomwalira iwe siidziwika.
SRD RASHID