[male vocals] Justin
kamasoba
Vubwi
MC
I
love
you
Victoria *
Verse 1*
Victoria,
zina
lako
limanipangitsa
kumwetulira
Mawu
ako
ndi
ngati
nyimbo
m'makutu
mwanga
Ndakuwona
ukugwira
ntchito
kwa
anthu
a
Vubwi
Ndipo
mtima
wanga
wasankha
iwe *
Chorus* *
Be
mine
Victoria,
be
mine* *
I
really
love
you,
it's
so
true* *
Mtima
wanga
na
wako* *
Univomere
ndikukonde* *
Be
mine
Victoria,
be
mine* *
Tiyende
pamozi
pa
mseu
kuti
uzibe
nikukonda* *
Ndikulonjeza
kukukonda* *
Kwa
masiku
onse
a
moyo
wanga* *
Verse 2*
Nikuziwa
uli
na
ntchito
yaikulu
Kuthandiza
makolo
bako,
kuthandiza
banja
lako
Koma
allow
me
nikhale
pambali
yako
Kukuthandiza,
kukukonda,
kukusamalira *
Bridge*
Ngati
ungandipatse
mwayi
Nikuwonetse
chikondi
chenicheni
Osati
mawu
chabe
Koma
zochita
tsiku
ndi
tsiku *
Outro* *
Victoria...
be
mine* 💚
Justin
kamasoba
i
love
you
so
much
Victoria