[male
vocals] (
Ad-libs:
Yehova
ndinu
wamkulu!
Amen!)
Oh,
ndili
pano
pamaso
panu,
Ndikulira
mwa
chikhulupiliro.
Tinabadwa
khumi
n'a
ziwiri
m'banja
limodzi,
Ine
ndili
namba 5
pakubadwa,
Chaka
cha
chikwi
chimodzi,
makumi
asanu
ndi
anayi,
September
pa
makumi
awiri
mphambu
zisanu
ndi
ziwiri,
Umoyo
unali
wovuta,
zaka
zokhala
m'manja
mwanu,
Ndikuyamikira
mmene
munandikonzera.
Ndilangizeni,
ndizuzuleni
osanditayilira,
Osandikwiyira
komanso
osandida,
ndine
mwana
wanu,
Ndilangizeni,
ndizuzuleni
osanditayilira,
Osandikwiyira
komanso
osandida,
ndine
mwana
wanu,
Ndilangizeni,
ndizuzuleni
osanditayilira,
Osandikwiyira
komanso
osandida,
ndine
mwana
wanu.
Munandiphunzitsa
sukulu,
ntchito
zamanja
m'manja,
Munandiphunzitsa
ulemu,
kulemekeza
anzanga,
Koma
lero
kodi
zaipira
pati
kuti
munditaye?
Mtima
wanga
ukupweteka,
ndikufuna
chitsogozo,
Mulungu
awone
pakati
pathu,
ndine
mwana
wanu.
Amama,
Adadi,
chonde
musandikwiyire,
Ndine
wochimwa,
ndine
wophonya,
koma
ndine
mwana
wanu,
Ndikufa
ndi
chisoni,
ndikufa
ndi
ndimaganizo,
Chonde
mverani
pempho
langa
lero!
Ndilangizeni,
ndizuzuleni
osanditayilira,
Osandikwiyira
komanso
osandida,
ndine
mwana
wanu,
Ndilangizeni,
ndizuzuleni
osanditayilira,
Osandikwiyira
komanso
osandida,
ndine
mwana
wanu,
Ndilangizeni,
ndizuzuleni
osanditayilira,
Osandikwiyira
komanso
osandida,
ndine
mwana
wanu.
Osanditayilira
amama,
Osandikwiyira
adadi,
Ndine
mwana
wanu,
nthawi
zonse,
Mulungu
alipo,
amve
kulira
kwanga.
Amen!
Nthawi
Zina
nimaganiza
kungozipha
chifukwa
coona
monga
MOYO
wanga
ndiopanda
phindu
Kolasi
Shadreck
Tembo
mwana
wanu