[male
vocals] *
Intro /
Shout*
Hey!
Hey!
Justin
Kamasoba!
Vubwi
MC
Zambia
yathu!
Vubwi
Constituency!
Tivote!
Tivote! *
Verse 1*
Banja
la
Zambia
lamva
kale
Nthawi
yafika
yoti
tisankhe
Mtsogoleri
wadziko
lonse
Wokhala
ndi
masomphenya
a
chitukuko *
President
Hakainde
Hichilema!*
Wanthu,
womvera,
wogwira
ntchito *
Verse 2*
Ku
Vubwi
kwathu
kuno
tiyeni
Tisankhe
mtsogoleri
wotikumbutsa *
MP
Honorable
Ackleo
Banda*
Wodziwa
mavuto
athu,
wokonzeka
kutitumikira
Ndi
iye
timanga
sukulu
ndi
zipatala
Ndi
iye
njira
zathu
zikukonzeka *
Pre-Chorus*
Komanso
tiyiwala
bwanji
Atsogoleri
akumidzi
kwathu *
Council
Chairperson*
ndi *
all
the
Councilors*
Ndiwo
manja
ndi
mapazi
a
chitukuko
Kuchokera
ku
ward
mpaka
ku
boma *
Tivote,
tiyende
patsogolo!*
Hakainde
Hichilema
President
wathu
Ackleo
Banda
MP
wathu
Chipiliro
kwenda
Council
Chair
ndi
ma
Councilors
onse
Pa 18
August...
Izi
ndi
Zathu!
Tivote,
tivote,
kuti
dziko
likule *
Verse 3*
Za
ulimi,
za
ana
asukulu
Za
achinyamata
ndi
ntchito
Za
madzi
aukhondo
ndi
magetsi
Zonse
zimatheka
tikasankha
atsogoleri
oyenera
Musakhale
kunyumba
pa
tsiku
la
mavoti
Lembani
X
yanu,
mawu
anu
ndi
mphamvu *
Bridge*
Zambia
ndi
ya
tonse
Vubwi
ndi
ya
tonse
Tisiyane
ndi
chipani,
tigwirizane
ndi
chitukuko
Kuyambira
President
mpaka
Councilor
Team
imodzi,
cholinga
chimodzi *
Final
Chorus +
Outro* *
Tivote
Hakainde
Hichilema!* *
Tivote
Ackleo
Banda!* *
Tivote
Chipliro
kwenda
Council
Chairperson!* *
Tivote
all
the
Councilors!* *
Tivote,
tiyende
patsogolo!*
Justin
Kamasoba
akuti:
Vubwi,
tatuluka!
Zambia,
tatuluka!
Osaiwala
Tino
kwa
chikoka,
msankha
moses,
BK
kwa
sando,
Amevi
Chris
ku
mbozi,
Patrick
sakala,
Abenja
uphawi
upatsa
nzeru
vubwi
Justine
kamasoba!
Pa 13
August
Vote
Ackleo
banda
vubwi
Constituency
na
Chipiliro
kwenda
council
chair
person