1 Mtima
wanga
uyamike
Mfumu
Yakumwambako;
Anandiwombola
ine
Nanditsuka
m'mtimamo.
Ife
tonse,
ife
tonse,
Tiyamike
Mlunguyo.
Ife
tonse,
ife
tonse,
Tiyamike
Mlunguyo. 2
Tiyamike
Mlungu
wathu
Kaamba
ka
chifundocho;
Nthawi
zonse
sasanduka
Mlungu
wathu
yemweyo.
Ife
tonse,
ife
tonse,
Tiyamike
Mlunguyo.
Ife
tonse,
ife
tonse,
Tiyamike
Mlunguyo. 3
Nthawi
zonse
monga
'Tate
Atisamaliratu,
Atisunga
m'manja
mwake,
Atipulumutsatu.
Ife
tonse,
ife
tonse,
Tiyamike
Mlunguyo.
Ife
tonse,
ife
tonse,
Tiyamike
Mlunguyo. 4
Anthu
a
mitundu
yonse,
Ndipo
a
Kumwambako,
Yamikani
Mlungu
wathu,
Ndiye
wakukomatu.
Anthu
onse,
anthu
onse,
Yamikani
Mlunguyo.
Anthu
onse,
anthu
onse,
Yamikani
Mlunguyo
Anthu
onse,
anthu
onse,
Yamikani
Mlunguyo.
Anthu
onse,
anthu
onse,
Yamikani
Mlunguyo
Done
by
Yotam
Mwale