[male
vocals] *
Intro /
Shout*
Awe!
Awe!
Justin
Kamasoba!
Mbozi
Ward!
Mukuti
ndani? *
BORNFACE
PHIRI!*
Mukuti
chiyani? *
NTCHITO!* *
Verse 1*
Banja
la
Mbozi
Ward
tamvani
Nthawi
yafika
yoti
tisankhe
Mtsogoleri
wodziwa
mavuto
athu
Wokhala
nafe,
woyenda
nafe *
Bornface
Phiri*
dzina
lake
Mtima
wa
chifundo,
dzanja
la
ntchito *
Verse 2*
Misewu
yathu
ikufuna
kukonzedwa
Ana
asukulu
akufuna
thandizo
Madzi
aukhondo
ndi
thanzi
lathu
Achinyamata
akufuna
mwayi
Bornface
wati "
ndili
pano"
Kumva
ndi
kuthetsa,
ndi
ntchito
yanga *
Pre-Chorus*
Sitingafune
munthu
wamawu
basi
Tikufuna
amene
amapita
ku
Council
Nkukaika
nkhani
zathu
patebulo *
Bornface
Phiri*
ndi
wokonzeka *
Chorus -
Call &
Response* *
Leader*:
Mbozi
Ward! *
Crowd*:
Bornface
Phiri! *
Leader*:
Tivote! *
Crowd*:
Tiyende
naye! *
All*: *
Bornface
Phiri,
Councilor
wathu!* *
Ntchito,
umodzi,
chitukuko!* *
Pa
ballot
pa 18
th,
lembani
dzina
lake*
Kuchokera
ku
chipanje,
mbozi ,
chafulu,
chimzimu,
kapandula,
songeya,
mpaka
ku
maumba
tivotere
bornface
phiri
Kuchokera
ku
sukulu
mpaka
ku
market
Mavuto
ndi
amodzi,
yankho
ndi
limodzi
Tiyeni
timuthandize
alowe
ku
Council
Kuti
Mbozi
Ward
chitukuko
chipite
patsogolo
Team
imodzi
ya
chitukuko
President
HH
kummwamba
akutithandiza
Ifenso
ku
ward
tisankhe
bwino *
Lembani
X,
lembani
Bornface!*
Justin
Kamasoba
akuyimba: *
Mbozi
Ward,
tatuluka!
Bornface
Phiri,
Ni
kwenyu*
Justin
kamasoba
vubwi
MC
Ackleo
banda
vubwi
Constituency
Chipiliro
kwenda
council
chair
Osaiwala
Amevi,
Chris,
Deus
former
councilor ,
wandasoni,
webby,
ku
chipanje,
Solomon,
chipisoni
azayero
ku
maumba
Justin
kamasoba