Frobits
🎵 A song made on Frobits

Rise Together

0:000:00
Download
Make your own song
Continues securely on the web
Lyrics

[male

vocals] *

Intro /

Shout*

Vubwi!

Vubwi!

Wathu

ndani? *

ACKLEO

BANDA!*

Wagwira

ntchito? *

INDE!* *

Verse 1 -

Roads*

Anthu

aku

Vubwi

tamvani

Honorable

wathu

wagwira

ntchito *

Anagula

ma

machines

a

misewu* *

Full

set*

kuti

misewu

imangidwe

Kuchokera

ku

mudzi

mpaka

ku

msika

Tsopano

magalimoto

akuyenda

bwino

Chitukuko

chafika *

Verse 2 -

Water &

Youth* *

Ma

water

schemes*

m’

midzi

yonse

Ana

ndi

amayi

sakuyenda

kutali

kukatapa

madzi *

Achinyamata*

anawapereka

ku *

driving

school*

Apa

ali

ndi

ma

layisensi,

ali

ndi

ufulu

olowa

nchito

komwe

alufuna

Ackleo

Banda

Salusankha

munthu

aliyense

Ackleo

aluthandiza

mosasankha

mbali

ku

ma

ward

onse

a

vubwi

Constituency *

Amayi

a

ma

club*

anawathandiza

Ndalama

ndi

zipangizo

kuti

mabizinesi

akule *

Akatswiri

a

nyimbo*

anawathandiza

kuti

vubwi

ikhala

map

Vubwi

tsopano

ili

ndi

mawu *

Mipikisano

ya

mpira

ndi

netball*

Amayiika

ndalama

kuti

achinyamata

asewere

Umodzi

ndi

chisangalalo

m’

dera

lathu

Kuti

achepetse

early

marriages

komaso

achinyamata

ku

ledzere

mowa *

Pre-Chorus*

Sikuti

malonjezo

okha

Ndi

ntchito

zomwe

tikuziona

Manja

ake

akumanga

Vubwi

Mtima

wake

uli

ndi

anthu *

Chorus -

Call &

Response* *

Leader*:

Vubwi

ikuti

chiyani? *

Crowd*:

ZIKOMO

ACKLEO! *

Leader*:

Tikufuna

ndani? *

Misewu

yabwino,

madzi

m’

midzi* *

Ntchito

kwa

achinyamata* *

Thandizo

kwa

amayi,

mpira,

nyimbo* *

Vubwi

tiyende

ndi

Ackleo

Banda!* *

Bridge*

Kuyambira

ku

maumba

mpaka

ku

choumba,

ku

nyakhoma

mpaka

ku

matemba

tivotere

ackleo

Banda

kuti

apitilize

chitukuko *

Ackleo

Banda* -

munthu

wa

anthu

Wogwira

ntchito,

osati

mawu *

Final

Chorus* *

Vubwi

yonse

imva* *

Misewu,

madzi,

masukulu* *

Achinyamata,

amayi,

masewera* *

Zonse

chifukwa

cha

Ackleo

Banda* *

Tiyeni

timupatse

vote

kuti

chitukuko

chipite

patsogolo* *

Vubwi

tiyende

naye!* *

Outro*

Justin

Kamasoba : *

Pa

tsiku

la

voti

musaiwale*

Ackleo

Banda* *

Kuti

ku

Vubwi

chitukuko

chipitirire

patsogolo!*

Justin

kamasoba

vubwi

MC

Justin

kamasoba

Timuvotere

ackleo

Banda

na

Chipiliro

kwenda

council

chair

person

More songs by Vmc Listen to songs created by others
FROBITS