[female
vocals] *
Intro /
Crowd*
Vubwi!
Mwakonzeka? *
TATI
CHITUKUKO!* *
TATI
MARGARET
MITI!* *
ABWERASO!
ABWERASO!* *
Verse 1*
ACKLEO
BANDA
akusiirani
ntchito
Vubwi
Boarding
School
yatha
kwasala
utsekula
Misewu
yayamba
kutseguka
Ku
chokera
mu
CDF
Mai
Margaret
mwamva
zofuna
zathu
Katipemphereni
miseu
kuli
a
president
Siti
kupumula
nthawi
ya
Ntchito
yayamba
kumene *
Pre-Chorus*
Tikufuna
madzi
ambiri
Tikufuna
misewu
yabwino
Tikufuna
ntchito
kwa
achinyamata
Ndani
angatibweretsere?
Mai
Margaret
miti *
Chorus* *
It's
time
for
development!* *
Mai
Margaret
abweraso!* *
Tiyende
patsogolo
ndi
iye* *
Vubwi
silingasiyidwe* *
It's
time
for
development!* *
Tivote
Mayi
wathu
kachiwiri* *
Kuti
chitukuko
chipitirire* *
MARGARET
ABWERASO!* *
Verse 2*
Amayi
Margaret
miti
mupitilize
upanga
chitukuko
ma
contructs
patsani
bana
wanu
kuno
kuno
vubwi
Bana
ambiri
afuna
nchito
osalola
kuti
nchito
azilowa
ndiobwera
kondani
wina
aliyense
ons
e
ndi
bana
banu
Achinyamata
ali
ndi
chiyembekezo
mwainu
komaso
atsikana
Ntchito
zambiri
zatsala
Kumanga
zipatala,
kumanga
ma
bridge,
nyumba
zamaticha,
ma
class
block
Kuti
timalize
zomwe
tayamba
Tifunika
Mai
Margaret
apitilize
chitukuko *
Bridge -
Call &
Response* *
Leader*:
It's
time
for
what? *
Crowd*:
DEVELOPMENT! *
Leader*:
Ndani
abweretse? *
Crowd*:
MAI
MARGARET
MITI! *
Leader*:
Liti? *
Crowd*:
Ninthawi
yake! *
Leader*:
azachita
chiyani? *
It's
time
for
development!* *
Mai
Margaret
abweraso!* *
Manja
athu
ali
mmwamba* *
It's
time
for
development!* *
Tiyende
ndi
UPND* *
It's
time
for
development!* *
Kuti
dziko
lathu
lipite
patsogolo* *
It's
time
for
development!* *
Mai
Margaret
abweraso!* *
It's
time
for
development!* *
Mai
Margaret
abweraso!* *
Manja
athu
ali
mmwamba* *
Vubwi
ikuti
INDE!* *
It's
time
for
development!* *
Tiyende
ndi
UPND* *
Kuti
dziko
lathu
lipite
patsogolo* *
MARGARET
ABWERASO!* *
Chifukwa
chitukuko
chiyenera
kupitirira* *
Tili
nanu
Mayi
wathu* *
Mulungu
adalitse
Vubwi* 🇿🇲
Leader:
One
Zambia?
Crowd:
one
nation!
Justin
kamasoba
vubwi
MC
Justin
kamasoba