Stephen Hamlets music productions_
*Verse 1*
Why is it that those we love don't care about us
They treat us bad no matter how much we love them
But daily bama tipotela ati "sindize choice yao" nga why baja
Bamene tikonda sibatikonda oye why chili so
*Chorus*
Nkani yama love imanindabwisa ine
Uja ukonda siyakukonda
Uja wamene siukonda diyeve akukonda × 4
*Verse 2*
Palya mumano uleti nasanga sweetie kena mumano kaleti
Aba nabo balaibepa abanabo balaimo
Palya mumano uleti nasanga soul mate kena mumano kaleti
Chakuposelamo inshita
*Chorus*
Nkani yama love imanindabwisa ine
Uja ukonda siyakukonda
Uja wamene siukonda diyeve akukonda × 4
*Verse 3 - New*
Ndalila mausiku, nkatemwa ndi mtima wonse
Nkapeleka zonse, koma iwe waseka chikondi changa
Ati "leka kumalira", koma ululu ndi wanga
Love is pain sometimes, when the heart you choose, chooses another
Baba God, why me? Nkafunika chiyani kuti undikonde?
Nkakhala mpweya wako, nkakhala chisangalalo chako
Koma iwe wasankha uja... uja osakukonda
*Final Chorus - Big*
Nkani yama love imanindabwisa ine
Uja ukonda siyakukonda
Uja wamene siukonda diyeve akukonda × 8
Eeeh, why chili so... why chili so... my heart is breaking
*Outro - Spoken*
Stephen Hamlets... nkani yama love... imanipweteka ine...