Frobits
🎵 A song made on Frobits

Mangingi: The People's Voice

0:000:00
Download
Reply with a song
Lyrics

Alfred Lungu, niosiyanako!!
James lungu, niosiyanako!
Charles Tembo NI BIG MACHINE!
2026 NIOSIYANAKO!!!
...............
Chorus
..............
A Menyani chino chaka nipati tivotela?
Ni pambale na spoon, ndiye pe tivotela !
A Menyani chino chaka nipati tivotela?
Ni pa mbale Napa sipuni ndiye pe tivotela ! haaaa ndiye pali Mangingi!
Tiyeni tonse tivotel Mangingi kuti malo wasu asianeko chifukwa Mangingi niosiyanako,
Chino chaka Nipa mbale!
Alfred lungu niosiyanako, uyu yeve ni big machine
Chino chaka Nipa mbale ndiye Pali chitukuko.
Tiyeni tivote Mangingi nimuthu wa mutima wa chikondi namutima wa wachitukuko chifukwa aziwa mabvuto a anthu amu manyane,
Mangingi azaleta ma market, ma machine monga opangila sausage, chimphunde, ma machine a malungu a nkhuku,
Mangingi azapanga ma comparative ya azimai ndi ma youth,
tiyeni tonse tivotele manging kuti malo anthu achinji,
Tiyeni tivotele mangingi kuti agedeze malo athu
Tivotele mangingi kuti ndala za cash for work anthu onse atengeko,
Tiyeni tivotele Alfred lungu kuti:
_ manjila agedeze
_ma bridge agedeze
_ma grant agedeze
_ma sikulu agedeze
Menyani ayi gedeze!
TIYENI TONSE TINYAMUKE, TIKAVOTE PA mbale na sipuni
Mangingi ni big machine, jelemani machine, Mangingi niyosiyanako,
mangingi ni big machine, jelemani machine!!

More songs by Alfredma Listen to songs created by others
FROBITS