(Upbeat
rhythmic
guitar
riff,
building
fast)
Alex
again
and
again
a
Mbuye
verani
pemphero
langa
ine
mwana
wan
a
Kuyesa
ndimayesa
ma
ganyu
ndimagwira
Koma
palibe
chimayenda
vuto
ndi
chiyani
mbuye
e
Mavuto
mngosayamba
banja
nalo
ndivuto
Anzanga
amandizonda
safuna
kukhala
nane
Kodi
pa
nkhope
panga
mwayi
palibe
yesu?
Kapena
ndine
chimwa
ngakoo
eee
yawe
aaaa
Yankhani
mbuye
wanga
ndinu
mwini
zose
eee
My
hands
are
tired
from
working,
yet
the
struggle
never
ends
Kodi
ndikalambire
mma
ganyu
yesuwe?
Chorus
Usalire
Musalire
tatontholani
mbuye
yesu
amaona
Musalire
Musalire
tatontholani
mwini
moyo
amalangana
pa
moyo
wako
Chofunika
mkumuyamika
kumukweza
kumuvera
Tsiku
Lina
azakuyankha
uzadabwa
pa
moyo
wakowe
aaaa
Musalire
tatontholani
eeee
Mwini
moyo
amalangana
aaaa
Amawona
amasunga
amasala
eeee (
Guitar
solo,
energetic
and
melodic)
Kapena
nchito
zanga
simukondwera
nazo
yawe
Njira
zanga
kapena
mza
mu
mdima
mbuye
Chuma
alinacho
koma
anachita
upanda
Chili
chose
chimawayendera
a
Amakhala
mosangalala
banja
losangalala
Kapena
Inu
mbuye
mumakondwera
Lesa
imwe
Nanga
bwanji
mumawadalisabe
ana
anu
akuvutika?
Mbuye
mbuye
wanga
ndilira
imwe
Lesa
Usalire
Musalire
tatontholani
mbuye
yesu
amaona
Musalire
Musalire
tatontholani
mwini
moyo
amalangana
pa
moyo
wako
Chofunika
mkumuyamika
kumukweza
kumuvera
Tsiku
Lina
azakuyankha
uzadabwa
pa
moyo
wakowe
aaaa
Musalire
tatontholani
eeee
Mwini
moyo
amalangana
aaaa
Amawona
amasunga
amasala
eeee
My
hands
are
tired
from
working,
yet
the
struggle
never
ends
Rap
Limba
mtima
mwana
wanga
ine
ndimakukonda
Chilichonse
ndimaona
ndipo
ndimavera
Palibe
chindivuta
kudalisa
iwe
mwana
Ukaziyendabe
usapaname
limbikabe
Sungilira
mawu
anga
komaso
malamuro
Lovenes
khwabe
hahahaha
Promise
mumba
Shana
vina
Shana
Berther
khwabe
praise
God
and
dance
Suvester
vina
vina
shanila
yesu
Ndombolo
yesu
aaaa
ndombolo
yawe
Isaac
I
see
you
hahahaha
Alicia
dance
ndombolo
yawe
Hillary
hahahaha
Praise
God
and
dance
ndombolo
yawe (
Fade
out
with
vibrant
rhumba
rhythm)