[male
vocals] (
Gentle
acoustic
guitar
strumming,
rhythmic
hand-claps,
soft
melodic
brass
swell) (
Gentle
acoustic
guitar
strumming,
rhythmic
hand-claps,
soft
melodic
brass
swell)
Wina
atikonda
ife,
Bwenzi
lathu
ndiyeyu;
Atifunafuna
ife,
Inde,
nthawi
zonsetu.
Chikondano
chakechi
Nchachikulukuludi.
Ndani
mwa
abale
athu
Akanatifera
'fe?
Koma
Yesu
m'malo
mwathu
Anapachikidwatu.
Anamnyoza
pansi
pano,
Bwenzi
la
ochimwawo;
Muulemerero
wake
Alikonda
Dzinali.
Timchimwira
kopambana,
Ndi
kumusautsa
'Ye,
Koma
Bwenzi
lathu
Yesu
Atikondakondabe.
Mtiphunzitse,
Mbuye
Yesu,
Tikondane
nanutu;
Tisaiwalire
konse
Bwenzi
lathu
ndinutu.
Konda
dzinalo
la
Yesu
Mwana
wosauka
'we;
Ndilo
lothandiza
anthu;
Khala
nalo
ponse
phee!
Dzina
la
Yesuyo
Nlokondwetsa
onsewo,
M'mwambamo
ponsepo
Litonthoza
m'mtimamo.
Konda
dzinalo
la
Yesu
M'moyo
mwako
monsemo;
M'mene
ulikuyesedwa,
Tchula
Dzina
lakelo.
Dzina
ili
ndi
lokoma
La
Mtetezi
wathuyo;
M'mene
adzatilandira
M'mwamba,
tidzakondwadi.
Mbuye
Yesu
timtamanda
Ndi
zinyimbo
zathuzo;
Mfumu
ya
mafumu
onse
Yesu
timayesadi.
Mbuye
wondipulumutsa
Mulandire
mtima
wanga,
Mwandipatsa
Mzimu
wanu
Womeretsa
zipatsomo.
Ndiye
Mzimu
Wakuyera
Atipatsa
ife
makhalidwe
Wofanana
naye
Yesu,
Anatsika
Kumwambako.
Naye
Mzimu
mndiphunzitse
Kukondwera
nsiku
zonse
Ndi
kukhala
ndi
mtendere
Osaderatu
nkhawa
'yi.
Mndithandize
kukondana
Ndikuthangatira
onse,
Ndi
kukhululukirabe
Akundichimwirawo.
Mndilimbitse
ndipirire
Osadandaula
konse,
Ndi
kulamulira
thupi
Ndi
zofuna
zakezo.
Kudzirala
ndi
kufatsa,
Inde,
zonse
muzikonda,
Mndiphunzitse
pondipatsa
Mzimu
wanu
Woyerawo.
Cholimbitsa
mtima
ndi
Chonditsogolera
M'njira
ya
Mulunguyo;
Ine
ndili
nacho.
M'Bukuli
ine
ndi
Onse
owerenga
Mawu
a
Mulunguwo,
Timapeza
moyo.
Dzinthu
zakumundazo
Zilimbitsa
thupi;
Zolembedwa
m'Bukumo
Zimadyetsa
mtima.
Ndikachimwa,
Bukuli
Lindiyambotsutsa;
Limanditonthoza
ndi
Mawu
a
mtendere.
Pakudera
nkhawa
'ne,
Pakuchita
mantha,
N'kawerenga
m'Bukuli
Lindipatsa
mphamvu.
Lindionetsera
'ne,
Chifuniro
chake
Cha
Mbuyanga
Yesuyo,
Ndikamvere
bwino.
Zonse
mwazilembamo,
Mzimu
Wakuyera,
Kuzimvera
zonsezo
Mundithangatire.
M'Buku
lakuyerali
Powerenga
ife,
Mbuye
mutipatsemo
Moyo,
moyo,
moyo.
Ukapenya
kwa
Yesu
uliko
moyoko,
Inde,
moyo
tsopanopanutu;
Wolakwira
upenye
kwa
Yesu
Mbuyeyo,
Kuwombola
naferatu
'we.
Ona!
Ona!
Onatu!
Kuli
moyo
kwa
yense
apenya
Yesuyo
Wakuferatu
pamtandapo.
Anasenza
pa
bwanji
uchimo
wonsewo,
Ngati
wanu
pa
Yesu
sulipo?
Bwanji
mwazi
wakhetsa
kutsuka
ifetu,
Ngati
uwu
sitikwanako?
Zilepheradi
zonse
kugula
moyowo,
Koma
mwazi
wa
Yesu
Mbuyeyo.
Khulupira
mwa
mphamvu
ya
Mlungu
wathuyi
Kuyeretsa
'we
m'mtimakomo!
Anathera
pamtanda
zintchito
zonsezi
Zowombola
mizimu
yathuyi;
Ndipo
yense
akadza
mokondwakondwadi
Moyo
apeza
kwa
Yesuko.
Sing'anga
'mkulu
ndiye
Yesu,
Mwana
wa
Mulungu;
Asangalatsa
achisoni,
Ali
wachifundo.
Dzina
la
Yesu
ndi
lokoma,
Dzina
la
Yesu
lipambana,
Dzina
lake
lakukonda,
Yesu,
inde
Yesu.
Zoipa
zakhululukidwa,
Yesu
amatero;
Tiyende
bwino
m'njira
yake,
Tilowemo
lero.
Nditama
Nsembe
ya
Mulungu,
Ndilandira
Yesu;
Ndikonda
dzinalo
labwino,
Dzina
lanu,
Yesu.
Akulu
inu
m'bwere
nonse,
Ana
inu
nomwe,
Ambuye
akuitanani,
Bvomerani
nonse. (
Gentle
acoustic
guitar
strumming,
rhythmic
hand-claps,
soft
melodic
brass
swell)
Wina
atikonda
ife,
Bwenzi
lathu
ndiyeyu;
Atifunafuna
ife,
Inde,
nthawi
zonsetu.
Chikondano
chakechi
Nchachikulukuludi.
Ndani
mwa
abale
athu
Akanatifera
'fe?
Koma
Yesu
m'malo
mwathu
Anapachikidwatu.
Anamnyoza
pansi
pano,