Frobits
🎵 A song made on Frobits

Rhythm of Praise

0:000:00
Download
Reply with a song
Lyrics

Verse 1
Mundimvere, Mbuye wanga
Nkana ine ndimalakwa,
Koma ndinu moyo wanga;
Ndine mlendo pansi pano,
Msanditaye m'dzanja lanu,
Mundisunge mwana wanu;
Mbuye, mkhale ndine.
Chorus
Mbuye....
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye......mkhale ndine.
Verse 2
Munafera ine kale
Kuti mukandimasule,
Lero lino mndinyamule;
Mbuye, mkhale ndine.
Mundidzze ndi chikondi,
Mndiyeretse m'mtima monse,
Chifuniro change mthyole;
Mbuye, mkhale ndine.
Chorus
Mbuye....
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye......mkhale ndine.
Verse 3
Imfa ikandifikira,
Inu ndidzakangamira;
Ndikalowa ine m'mdima,
Mbuye, mkhale ndine.
Chorus
Mbuye....
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye......mkhale ndine.
Mbuye....
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye, mkhale ndine.
Mbuye......mkhale ndine.

More songs by Mike Listen to songs created by others
FROBITS