[male vocals] Oh,
Amen,
tamikani
Ambuye
Yesu
ndi
mwala
wamtengo
wapatali,
tikuyamikila
Ine
Simiyoni
David
Banda,
ndiyima
pano
Ndi
mtima
wodzala
ndi
chiyamikilo
chachikulu
Pa
utsogoleri
wabwino
umene
muli
nawo
Mu
mpingo
wathu
wa
CMML
Mgawa,
muli
madalitso
Ambuye
akuyang'anani,
akudalitseni
mwa
chifundo
Nthawi
zonse,
pamanja
panu
pali
mphamvu
Tikuyamikila
atsogoleri,
ankhosa
a
Ambuye
Elder
David
Banda,
Elder
Charles
Mashowo
Elder
Mussa
Tembo,
ndi
Elder
Mabvuto
Tembo
Ambuye
akudalitseni,
utumiki
wanu
upite
pasogolo
Yes
Lord,
Amen,
utumiki
wanu
upite
pasogolo
Elder
Isaac
Phiri,
Elder
Cryson
Nkhoma
Elder
Peter
Nkhoma,
ndi
Elder
Ezekiel
Phiri
Mumatsogolera
anthu
ndi
chikondi
chochokera
kwa
Mulungu
Kuyenda
m'njira
ya
choonadi,
popanda
mantha
Ntchito
imene
mukugwira,
ili
ndi
mphotho
yakumwamba
Tamikani
Ambuye,
pakuti
ntchito
yanu
ikuwala
Tikuyamikila
atsogoleri,
ankhosa
a
Ambuye
Elder
David
Banda,
Elder
Charles
Mashowo
Elder
Mussa
Tembo,
ndi
Elder
Mabvuto
Tembo
Ambuye
akudalitseni,
utumiki
wanu
upite
pasogolo
Yes
Lord,
Amen,
utumiki
wanu
upite
pasogolo
Zikomo
chifukwa
cha
kuona
mtima
Zikomo
chifukwa
cha
kupirira
kwanu
Ambuye
awonjezere
mphamvu
m'miyoyo
yanu
Kuti
utumiki
uwu
ukhale
mpaka
muyaya
Glory
to
God,
mwa
atsogoleri
athu!
Simiyoni
David
Banda
akupembedza
lero
Kuti
Mulungu
akusungeni
m'chikondi
chake
Nthawi
zonse
muzikhala
zitsanzo
zabwino
Kuti
mpingo
ukule,
mzimu
ukhale
wolimba
Amen,
Amen,
tikuyamikila
kwanu
Tikuyamikila
atsogoleri,
ankhosa
a
Ambuye
Elder
David
Banda,
Elder
Charles
Mashowo
Elder
Mussa
Tembo,
ndi
Elder
Mabvuto
Tembo
Ambuye
akudalitseni,
utumiki
wanu
upite
pasogolo
Yes
Lord,
Amen,
utumiki
wanu
upite
pasogolo
Ambuye
akudalitseni
nonse
atsogoleri
Utumiki
wanu
upite
pasogolo,
Amen
Zikomo,
zikomo,
kwa
nonse
Yes
Lord,
utumiki
wanu
upite
pasogolo.