[male vocals] Ndikulira
imfa
ya
mwana
wanga
Feva,
anali
mwana
wanga
wapamtima,
ndigwire
mtengo
wanji
Yehova,
mzimu
wa
mwana
wanga
upeze
mtendere 😭😭😭
ndidzakuphonya
mpaka
kalekale
Feva,
anali
mwana
wanga
amene
ndinkamukonda
kwambiri,
pumula
mu
mtendere ✌️
ndikukumbukira
kwambiri
mwana
wanga,
ndine
bambo
ako
Feva,
mwana
wanga
Mulungu
tithandizeni,
ndikulira 😭😭
mwana
wanga
Feva
undikumbuke
kumene
uli,
mwana
wanga
Favor
pomaliza
nyimbo
yanga
ndine
Mati
Kazuma
Mwase
Boy
ndipo
ndipereke
moni
kwa
anzanga
Chasefu
Soldier,
Moses
Chulu
ndakuona,
Balantha
Village
Lundazi